Miyambo 1:3 - Buku Lopatulika3 kulandira mwambo wakusamalira machitidwe, chilungamo, chiweruzo ndi zolunjika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 kulandira mwambo wakusamalira machitidwe, chilungamo, chiweruzo ndi zolunjika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 kuti alandire mwambo wochita zinthu mwanzeru, akhale angwiro, achilungamo ndi osakondera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 kuti alandire malangizo othandiza kuti achite zinthu mwanzeru, akhale wangwiro, wachilungamo ndiponso wosakondera. Onani mutuwo |