Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 1:2 - Buku Lopatulika

2 Kudziwa nzeru ndi mwambo; kuzindikira mau ozindikiritsa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Kudziwa nzeru ndi mwambo; kuzindikira mau ozindikiritsa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ngothandiza kuti anthu adziŵe nzeru ndi mwambo, kuti amvetse mau a matanthauzo ozama,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndi yothandiza kuti munthu adziwe nzeru ndi malangizo; kuti amvetse mawu a matanthauzo ozama;

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 1:2
13 Mawu Ofanana  

Kuopa Yehova ndiko mwambo wanzeru; ndipo chifatso chitsogolera ulemu.


Kodi kulandira nzeru sikupambana ndi golide, kulandira luntha ndi kusankhika koposa siliva?


Kodi bwanji mtengo wogulira nzeru uli m'dzanja la chitsiru, popeza wopusa alibe mtima?


Tamvera uphungu, nulandire mwambo, kuti ukhale wanzeru pa chimaliziro chako.


Pamenepo udzazindikira chilungamo ndi chiweruzo, zolunjika ndi mayendedwe onse abwino.


Ananu, mverani mwambo wa atate, nimutchere makutu mukadziwe luntha;


Nena kwa nzeru, Ndiwe mlongo wanga; nutche luntha mbale wako.


Imvani mwambo, mukhale anzeru osaukana.


Achibwana inu, chenjerani, opusa inu, khalani ndi mtima wozindikira;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa