Mateyu 28:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo iwo analandira ndalamazo, nachita monga anawalangiza: ndipo mbiri iyo inabuka mwa Ayuda, kufikira lero lomwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo iwo analandira ndalamazo, nachita monga anawalangiza: ndipo mbiri iyo inabuka mwa Ayuda, kufikira lero lomwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Alonda aja atalandira ndalama zija, adachitadi monga momwe adaaŵauzira. Motero mbiri imeneyi idawanda pakati pa Ayuda mpaka lero lino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Pamenepo alondawo anatenga ndalamazo nachita monga mmene anawuzidwira. Ndipo mbiri iyi inawanda pakati pa Ayuda mpaka lero lino. Onani mutuwo |