Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 27:65 - Buku Lopatulika

65 Pilato anati kwa iwo, Tengani alonda; mukani, kasungeni monga mudziwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

65 Pilato anati kwa iwo, Tengani alonda; mukani, kasungeni monga mudziwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

65 Pilato adaŵauza kuti, “Paja alonda muli nawo. Pitani, kalondeni pamandapo monga mukudziŵira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

65 Pilato anayankha kuti, “Tengani mlonda kalondereni monga mudziwira.”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 27:65
5 Mawu Ofanana  

Indedi, kuzaza kwake kwa munthu kudzakulemekezani; chotsalira cha kuzazaku mudzachiletsa.


Kulibe nzeru ngakhale luntha ngakhale uphungu wotsutsana ndi Yehova.


Chifukwa chake mulamule kuti asindikize pamandapo, kufikira tsiku lachitatulo, kuti kapena ophunzira ake angadze, nadzamuba Iye, nadzanena kwa anthu, kuti Iye anauka kwa akufa: ndipo chinyengo chomaliza chidzaposa choyambacho.


Ndipo iwo anamuka, nasunga manda, nasindikizapo chizindikiro pamwalapo, iwo pamodzi ndi alondawo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa