Mateyu 27:55 - Buku Lopatulika55 Ndipo anali pomwepo akazi ambiri, akuyang'anira patali, omwe anatsata Yesu kuchokera ku Galileya, namatumikira Iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201455 Ndipo anali pomwepo akazi ambiri, akuyang'anira patali, omwe anatsata Yesu kuchokera ku Galileya, namatumikira Iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa55 Patali poteropo padaali azimai ambiri akungoyang'anitsitsa. Iwoŵa ndi amene adaatsatira Yesu kuchokera ku Galileya ndi kumamtumikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero55 Amayi ambirimbiri amene ankasamalira Yesu ankaonerera ali patali. Iwo anamutsatira Yesu kuchokera ku Galileya. Onani mutuwo |