Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 27:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo anaika pamwamba pamutu pake mlandu wake wolembedwa: UYU NDI YESU MFUMU YA AYUDA.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo anaika pamwamba pamutu pake mlandu wake wolembedwa: UYU NDI YESU MFUMU YA AYUDA.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Pamwamba pa mutu wake adaalembapo mau osonyeza mlandu womuphera, akuti, “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Pamwamba pa mutu wake analembapo mawu osonyeza mlandu wake akuti, “uyu ndi yesu, mfumu ya ayuda.”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 27:37
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo anapachika pamodzi ndi Iye achifwamba awiri, mmodzi kudzanja lamanja, ndi wina kulamanzere.


Anapulumutsa ena, sangathe kudzipulumutsa yekha. Ndiye mfumu ya Aisraele; atsike tsopano pamtandapo, ndipo tidzamkhulupirira Iye.


Ndipo lembo la mlandu wake linalembedwa pamwamba, MFUMU YA AYUDA.


Ndipo kunalinso lembo pamwamba pake, ndilo: UYU NDIYE MFUMU YA AYUDA.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa