Mateyu 27:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo anavula malaya ake, namveka malaya ofiira achifumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo anavula malaya ake, namveka malaya ofiira achifumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Adamuvula zovala zake, namuveka chovala chofiira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Anamuvula malaya ake namuveka Iye malaya ofiira aufumu. Onani mutuwo |