Mateyu 26:38 - Buku Lopatulika38 Pamenepo ananena kwa iwo, Moyo wanga uli wozingidwa ndi chisoni cha kufika nacho kuimfa; khalani pano muchezere pamodzi ndi Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Pamenepo ananena kwa iwo, Moyo wanga uli wozingidwa ndi chisoni cha kufika nacho kuimfa; khalani pano muchezere pamodzi ndi Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Adaŵauza kuti, “Mumtima mwanga muli chisoni chachikulu chofa nacho. Inu khalani pompano, komatu mukhale maso pamodzi nane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Pamenepo anawawuza kuti, “Moyo wanga uli ndi chisoni chofa nacho. Khalani pano ndipo dikirani pamodzi ndi Ine.” Onani mutuwo |