Mateyu 25:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo itapita nthawi yaikulu, anabwera mbuye wa akapolo awo, nawerengera nao pamodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo itapita nthawi yaikulu, anabwera mbuye wa akapolo awo, nawerengera nao pamodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 “Patapita nthaŵi yaitali, mbuye wao uja adabwerako naŵaitana antchito ake aja kuti amufotokozere za zimene adaachita ndi ndalama zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Patapita nthawi yayitali, mbuye wa antchitowo anabwera nawayitana kuti afotokoze chimene anachita ndi ndalama zija. Onani mutuwo |