Mateyu 25:18 - Buku Lopatulika18 Koma uyo amene analandira imodziyo anamuka, nakumba pansi, naibisa talente ya mbuye wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma uyo amene analandira imodziyo anamuka, nakumba pansi, naibisa talente ya mbuye wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Koma amene adaalandira ndalama imodzi uja, adapita nakaikumbira pansi ndalama ya mbuye wake ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Koma munthu amene analandira 1,000 uja, anapita nakumba dzenje nabisapo ndalama ya mbuye wake. Onani mutuwo |