Mateyu 25:11 - Buku Lopatulika11 Koma pambuyo pake anadzanso anamwali enawo, nati, Mbuye, mbuye, mutitsegulire ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma pambuyo pake anadzanso anamwali enawo, nati, Mbuye, Mbuye, mutitsegulire ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Kenaka m'mbuyomwalendo anamwali ena aja nawonso adabwera nati, ‘Bwana, Bwana, titsekulireni!’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Pambuyo pake enawo anabwera nati, ‘Ambuye! Ambuye! Titsekulireni!’ Onani mutuwo |