Mateyu 23:36 - Buku Lopatulika36 Indetu ndinena kwa inu, Zinthu zonse izi zidzafika pa mbadwo uwu wamakono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Indetu ndinena kwa inu, Zinthu zonse izi zidzafika pa mbadwo uwu wamakono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Ndithu ndikunenetsa kuti chilango cha zonsezi chidzaŵagwera ndithu anthu amakonoŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Zoonadi, ndikuwuzani kuti zonsezi zidzafika pa mʼbado uno. Onani mutuwo |