Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 23:24 - Buku Lopatulika

24 Atsogoleri akhungu inu, akukuntha udzudzu, koma mumeza ngamira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Atsogoleri akhungu inu, akukuntha udzudzu, koma mumeza ngamira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Inu atsogoleri akhungu, mumasuza zakumwa zanu kuti muchotsemo kanchenche, koma mumameza ngamira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Atsogoleri akhungu inu! Mumachotsa kantchentche mu chakumwa chanu koma mumameza ngamira.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 23:24
11 Mawu Ofanana  

Pakuti iwo amene atsogolera anthuwa, ndiwo awasokeretsa; ndipo iwo amene atsogoleredwa nao aonongeka.


Kawalekeni iwo, ali atsogoleri akhungu. Ndipo ngati wakhungu amtsogolera wakhungu, onse awiri adzagwa m'mbuna.


Ndiponso ndinena kwa inu, Nkwapafupi kuti ngamira ipyole diso la singano, koposa mwini chuma kulowa Ufumu wa Kumwamba.


Tsoka inu, atsogoleri akhungu, amene munena, Amene aliyense akalumbira kutchula Kachisi, palibe kanthu; koma amene akalumbira kutchula golide wa Kachisi, wadzimangirira.


Kapena udzati bwanji kwa mbale wako, Tandilola ndichotse kachitsotso m'diso lako; ndipo ona, mtandawo ulimo m'diso lakoli.


Pamenepo anamtenga Yesu kuchokera kwa Kayafa kupita ku Pretorio; koma munali mamawa; ndipo iwo sanalowe ku Pretorio, kuti angadetsedwe, koma kuti akadye Paska.


Pomwepo anafuulanso, nanena, Si uyu, koma Barabasi. Koma Barabasi anali wachifwamba.


Ndipo dziko linathandiza mkaziyo, ndi dziko linatsegula m'kamwa mwake, nilinameza madzi a mtsinje amene chinjoka chinalavula m'kamwa mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa