Mateyu 22:28 - Buku Lopatulika28 Chifukwa chake m'kuuka kwa akufa, iye adzakhala mkazi wa yani wa asanu ndi awiriwo? Pakuti onse anakhala naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Chifukwa chake m'kuuka kwa akufa, iye adzakhala mkazi wa yani wa asanu ndi awiriwo? Pakuti onse anakhala naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Nanga tsono pa tsiku lodzauka akufa, mwini mkaziyo adzakhala utiwuti pakati pa abale asanu ndi aŵiri aja, popeza kuti onsewo adaamkwatirapo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Tsopano, kodi akadzaukitsidwa adzakhala mkazi wa ndani mwa asanu ndi awiriwa popeza aliyense anamukwatirapo?” Onani mutuwo |