Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 21:45 - Buku Lopatulika

45 Ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi, pakumva mafanizo ake, anazindikira kuti alikunena za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi, pakumva mafanizo ake, anazindikira kuti alikunena za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 Pamene akulu a ansembe ndi Afarisi adamva mafanizo ameneŵa a Yesu, adazindikira kuti ankanena iwowo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 Akulu a ansembe ndi Afarisi atamva mafanizo a Yesu, anadziwa kuti ankanena iwo.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 21:45
6 Mawu Ofanana  

Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sabata.


Ndipo Iye anawauzira zinthu zambiri m'mafanizo, nanena, Onani, wofesa anatuluka kukafesa mbeu.


Ndipo iye wakugwa pamwala uwu adzaphwanyika; koma pa iye amene udzamgwera, udzampera iye.


Ndipo pamene anafuna kumgwira, anaopa makamu a anthu, chifukwa anamuyesa mneneri.


Ndipo mmodzi wa achilamulo anayankha, nanena kwa Iye, Mphunzitsi, ndi kunena izi, mutitonza ifenso.


Ndipo alembi ndi ansembe aakulu anafunafuna kumgwira ndi manja nthawi yomweyo; ndipo anaopa anthu; pakuti anazindikira kuti ananenera pa iwo fanizo ili.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa