Mateyu 21:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anadza kwa winayo, natero momwemo. Ndipo iye anavomera, nati, Ndipita mbuye; koma sanapite. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anadza kwa winayo, natero momwemo. Ndipo iye anavomera, nati, Ndipita mbuye; koma sanapite. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Bambo uja adapita kwa mwana wina uja, nakamuuza mau omwe aja. Iyeyo adati, ‘Chabwino atate,’ koma sadapite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 “Kenaka abambowo anapita kwa mwana winayo nanena chimodzimodzi. Iye anayankha kuti, ‘Ndipita abambo,’ koma sanapite. Onani mutuwo |