Mateyu 20:33 - Buku Lopatulika33 Ananena kwa Iye, Ambuye, kuti maso athu apenye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ananena kwa Iye, Ambuye, kuti maso athu apenye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Iwo aja adati, “Ambuye, tikufuna kuti tizipenya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Anamuyankha nati, “Ambuye, tikufuna tione!” Onani mutuwo |