Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 20:27 - Buku Lopatulika

27 ndipo aliyense amene akafuna kukhala woyamba mwa inu, adzakhala kapolo wanu:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 ndipo amene aliyense akafuna kukhala woyamba mwa inu, adzakhala kapolo wanu:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Ndipo aliyense wofuna kukhala mtsogoleri pakati panu, akhale kapolo wanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Ndipo aliyense amene akufuna kukhala woyamba akhale kapolo wanu.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 20:27
12 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake yense amene adzichepetsa yekha monga kamwana aka, yemweyo ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba.


Sikudzakhala chomwecho kwa inu ai; koma aliyense amene akafuna kukhala wamkulu mwa inu, adzakhala mtumiki wanu;


monga Mwana wa Munthu sanadze kutumikiridwa koma kutumikira, ndi kupereka moyo wake dipo la anthu ambiri.


Koma sipadzatero ndi inu; komatu iye ali wamkulu mwa inu, akhale ngati wamng'ono; ndi iye ali woyamba, akhale ngati wotumikira.


Ine ndili wamangawa wa Agriki ndi wa akunja, wa anzeru ndi wa opusa.


Pakuti ndiyesa kuti sindinaperewere konse ndi atumwi oposatu.


Ndipo ndidzapereka ndi kuperekedwa konse chifukwa cha miyoyo yanu mokondweratu. Ngati ndikonda inu kochuluka koposa, kodi ndikondedwa kochepa?


Pakuti tilalikira si za ife tokha, koma Yesu Khristu Ambuye, ndi ife tokha akapolo anu, chifukwa cha Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa