Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 15:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Anthu onsewo adadya mpaka kukhuta. Adatola zotsala, nkudzaza madengu asanu ndi aŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Onse anadya ndipo anakhuta. Pomaliza ophunzira anatolera zotsalira nadzaza madengu asanu ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 15:37
10 Mawu Ofanana  

Potero anawagawira, nadya, nasiyapo, monga mwa mau a Yehova.


Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.


Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'chipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu?


Ndipo anadyawo anali amuna zikwi zinai kuwaleka akazi ndi ana.


Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, ndipo eni chuma anawachotsa opanda kanthu.


koma ophunzira ake anamtenga usiku, nampyoletsa palinga, namtsitsa mu dengu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa