Mateyu 14:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Petro anamyankha Iye nati, Ambuye, ngati ndinutu, mundiuze ndidze kwa Inu pamadzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Petro anamyankha Iye nati, Ambuye, ngati ndinutu, mundiuze ndidze kwa Inu pamadzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Apo Petro adati, “Ambuye, ngati ndinudi, tandiwuzani kuti ndibwere kwa Inu pamadzipo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Petro anayankha nati, “Ambuye ngati ndinu, mundiwuze ndibwere kuli inuko pa madzipo.” Onani mutuwo |