Mateyu 12:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo anatambalitsa dzanja lake pa ophunzira ake, nati, Penyani amai wanga ndi abale anga! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo anatambalitsa dzanja lake pa ophunzira ake, nati, Penyani amai wanga ndi abale anga! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Atatero, adaloza ophunzira ake nati, “Inetu amai anga ndi abale anga ndi aŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Ndipo akuloza ophunzira ake, Iye anati, “Awa ndiwo amayi anga ndi abale anga. Onani mutuwo |