Mateyu 12:37 - Buku Lopatulika37 Pakuti udzayesedwa wolungama ndi mau ako, ndipo ndi mau ako omwe udzatsutsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Pakuti udzayesedwa wolungama ndi mau ako, ndipo ndi mau ako omwe udzatsutsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Mwakuti chifukwa cha mau ako omwe mlandu udzakukomera kapena kukuipira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Pakuti ndi mawu anu mudzapezeka osalakwa ndiponso ndi mawu anu mudzapezeka olakwa.” Onani mutuwo |