Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 98:8 - Buku Lopatulika

8 mitsinje iombe m'manja; mapiri afuule pamodzi mokondwera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 mitsinje iombe manja; mapiri afuule pamodzi mokondwera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Mitsinje iwombe m'manja, mapiri aimbe pamodzi mwachimwemwe

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Mitsinje iwombe mʼmanja mwawo, mapiri ayimbe pamodzi mwachimwemwe;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 98:8
7 Mawu Ofanana  

Atatero, anatulutsa mwana wa mfumu, namuika korona, nampatsa buku la umboni, namlonga ufumu, namdzoza, naomba m'manja, nati, Mfumu ikhale ndi moyo.


Ombani m'manja, mitundu yonse ya anthu; fuulirani kwa Mulungu ndi liu la kuimbitsa.


Munalenga kumpoto ndi kumwera; Tabori ndi Heremoni afuula mokondwera m'dzina lanu.


Muli nao mkono wanu wolimba; m'dzanja mwanu muli mphamvu, dzanja lamanja lanu nlokwezeka.


Mitsinje ikweza, Yehova, mitsinje ikweza mkokomo wao; mitsinje ikweza mafunde ao.


Pakuti inu mudzatuluka ndi kukondwa, ndi kutsogozedwa ndi mtendere; mapiri ndi zitunda, zidzaimba zolimba pamaso panu, ndi mitengo yonse ya m'thengo idzaomba m'manja mwao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa