Masalimo 98:7 - Buku Lopatulika7 Nyanja ifuule ndi kudzala kwake; dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Nyanja ifuule ndi kudzala kwake; dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zam'menemo, dziko lifuule pamodzi ndi anthu onse am'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zili mʼmenemo, dziko lonse ndi onse amene amakhala mʼmenemo. Onani mutuwo |