Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 98:6 - Buku Lopatulika

6 Fuulani pamaso pa Mfumu Yehova, ndi mbetete ndi liu la lipenga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Fuulani pamaso pa Mfumu Yehova, ndi mbetete ndi liu la lipenga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Imbirani Chauta Mfumu, imbani molimbika ndi malipenga ndi mbetete.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 ndi malipenga ndi kuliza kwa nyanga ya nkhosa yayimuna fuwulani mwachimwemwe pamaso pa Yehova Mfumu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 98:6
9 Mawu Ofanana  

Momwemo Aisraele onse anakwera nalo likasa la chipangano la Yehova ndi kufuula, ndi kumveka kwa lipenga, ndi mphalasa, ndi nsanje zomveketsa, ndi zisakasa, ndi azeze.


Ndipo analumbira kwa Yehova ndi mau aakulu, ndi kufuula ndi mphalasa ndi malipenga.


Nanena Hezekiya kuti apereke nsembe yopsereza paguwa la nsembe. Ndipo pakuyamba nsembe yopsereza, inayambanso nyimbo ya Yehova ndi malipenga, pamodzi ndi zoimbira za Davideyo mfumu ya Israele.


Pomwepo Mfumuyo idzanena kwa iwo a kudzanja lake lamanja, Idzani kuno inu odalitsika a Atate wanga, lowani mu Ufumu wokonzedwera kwa inu pa chikhazikiro chake cha dziko lapansi:


Ndipo ali nalo pa chovala chake ndi pa ntchafu yake dzina lolembedwa, MFUMU YA MAFUMU, NDI MBUYE WA AMBUYE.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa