Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 97:12 - Buku Lopatulika

12 Kondwerani mwa Yehova, olungama inu; ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Kondwerani mwa Yehova, olungama inu; ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Inu ndi anthu a Chauta, kondwerani mwa iye, ndipo mumthokoze potchula dzina lake loyera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Kondwerani mwa Yehova Inu olungama ndipo tamandani dzina lake loyera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 97:12
9 Mawu Ofanana  

Imbirani Yehova, inu okondedwa ake, ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake.


Pakuti mkwiyo wake ukhala kanthawi kokha; koma kuyanja kwake moyo wonse. Kulira kuchezera, koma mamawa kuli kufuula kokondwera.


Sekerani mwa Yehova, ndimo kondwerani inu olungama mtima; ndipo fuulani mokondwera nonsenu oongoka mtima.


Mulungu walankhula m'chiyero chake; ndidzakondwerera, ndidzagawa Sekemu, ndidzayesa muyeso chigwa cha Sukoti.


Kondwerani mwa Ambuye nthawi zonse: ndibwerezanso kutero, kondwerani.


Pakutitu iwo anatilanga masiku owerengeka monga kudawakomera; koma Iye atero, kukatipindulitsa, kuti tikalandirane nao pa chiyero chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa