Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 95:9 - Buku Lopatulika

9 Pamene makolo anu anandisuntha, anandiyesa, anapenyanso chochita Ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pamene makolo anu anandisuntha, anandiyesa, anapenyanso chochita Ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 pamene makolo anu adandiputa mondiyesa ngakhale anali ataona ntchito zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kumene makolo anu anandiyesa ndi kundiputa, ngakhale anaona zimene Ine ndinazichita.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 95:9
8 Mawu Ofanana  

Koma anamuyesa napikisana ndi Mulungu Wam'mwambamwamba, osasunga mboni zake;


popeza anthu onse awa amene adaona ulemerero wanga, ndi zizindikiro zanga, ndidazichita mu Ejipito ndi m'chipululu, koma anandiyesa Ine kakhumi aka, osamvera mau anga;


Sindikadachita mwa iwo ntchito zosachita wina, sakadakhala nalo tchimo; koma tsopano anaona, nada Ine ndi Atate wanganso.


Kapena tisayese Ambuye, monga ena a iwo anayesa, naonongeka ndi njoka zija.


Musamayesa Yehova Mulungu wanu, monga munamyesa mu Masa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa