Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 95:4 - Buku Lopatulika

4 Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lake; chuma cha m'mapiri chomwe ndi chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lake; chuma cha m'mapiri chomwe ndi chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Maziko ozama a dziko lapansi ali m'manja mwake. Mapiri aatali omwe ngakenso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mʼmanja mwake muli maziko ozama a dziko lapansi, ndipo msonga za mapiri ndi zake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 95:4
11 Mawu Ofanana  

Akapita, nakatsekera, nakatulutsa bwalo la mlandu, adzamletsa ndani?


Ndiye amene asuntha mapiri, osachidziwa iwo, amene amagubuduza mu mkwiyo wake.


Chilichonse chimkonda Yehova achichita, kumwamba ndi padziko lapansi, m'nyanja ndi mozama monse.


Mwampatsa iye chikhumbo cha mtima wake, ndipo simunakane pempho la milomo yake.


Ndinu amene mukhazikitsa mapiri ndi mphamvu yanu; pozingidwa nacho chilimbiko.


Inu, amene munationetsa nsautso zambiri ndi zoipa, mudzatipatsanso moyo, ndi kutitenganso munsi mwa dziko.


Mapiri anasungunuka ngati sera pamaso pa Yehova, pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi.


Ndi mapiri adzasungunuka pansi pa Iye, ndi zigwa zidzang'ambika, ngati sera pamoto, ngati madzi otsanulidwa potsetsereka.


Mapiri agwedezeka chifukwa cha Iye, ndi zitunda zisungunuka; ndi dziko lapansi likwezeka pamaso pake, ndi maiko ndi onse okhala m'mwemo.


Mapiri anakuonani, namva zowawa; chigumula cha madzi chinapita; madzi akuya anamveketsa mau ake, nakweza manja ake m'mwamba.


Anaimirira, nandengulitsa dziko lapansi; anapenya, nanjenjemeretsa amitundu; ndi mapiri achikhalire anamwazika, zitunda za kale lomwe zinawerama; mayendedwe ake ndiwo a kale lomwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa