Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 95:2 - Buku Lopatulika

2 Tidze nacho chiyamiko pamaso pake, timfuulire Iye mokondwera ndi nyimbo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Tidze nacho chiyamiko pamaso pake, timfuulire Iye mokondwera ndi nyimbo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Tiyeni, tikafike pamaso pake, tikamthokoze, tiyeni tifuule kwa Iye ndi chimwemwe, timuimbire nyimbo zotamanda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Tiyeni tibwere pamaso pake ndi chiyamiko ndipo mupembedzeni Iyeyo ndi zida zoyimbira ndi nyimbo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 95:2
11 Mawu Ofanana  

Tumikirani Yehova ndi chikondwerero: Idzani pamaso pake ndi kumuimbira mokondwera.


Lowani kuzipata zake ndi chiyamiko, ndi kumabwalo ake ndi chilemekezo: Myamikeni; lilemekezeni dzina lake.


Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.


Ukani Yehova, Mumtsekereze, mumgwetse, landitsani moyo wanga kwa woipa ndi lupanga lanu;


Ndipo ukuzingeni msonkhano wa anthu; ndipo pamwamba pao mubwerere kunka kumwamba.


Utsani salimo, bwera nakoni kalingaka, zeze wokondwetsa pamodzi ndi chisakasa.


Fuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi; kuwitsani ndi kufuulira mokondwera; inde, imbirani zomlemekeza.


Ndidzafika kwa Yehova ndi chinai, ndi kuwerama kwa Mulungu Wam'mwamba? Kodi ndifike kwa Iye ndi nsembe zopsereza, ndi anaang'ombe a chaka chimodzi?


ndi kudzilankhulira nokha ndi masalimo, ndi mayamiko, ndi nyimbo zauzimu, kuimbira ndi kuimba m'malimba Ambuye mumtima mwanu;


Kodi wina wa inu akumva zowawa? Apemphere. Kodi wina asekera? Aimbire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa