Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 94:22 - Buku Lopatulika

22 Koma Yehova wakhala msanje wanga; ndi Mulungu wanga thanthwe lothawirapo ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Koma Yehova wakhala msanje wanga; ndi Mulungu wanga thanthwe lothawirapo ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Koma Chauta wasanduka linga langa londiteteza, Mulungu ndiye thanthwe langa lothaŵirako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Koma Yehova wakhala linga langa, ndipo Mulungu ndiye thanthwe limene ndimathawirako.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:22
10 Mawu Ofanana  

Yehova ndiye thanthwe langa, ndi linga langa, ndi Mpulumutsi wanga; Mulungu wanga, ngaka yanga, ndidzakhulupirira Iye; chikopa changa, nyanga ya chipulumutso changa, msanje wanga.


Inu, mphamvu yanga, ndidzakulindirani; pakuti Mulungu ndiye msanje wanga.


Iye yekhayo ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa; msanje wanga, sindidzagwedezeka kwakukulu.


Iye yekhayo ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, msanje wanga, sindidzagwedezeka.


Khulupirirani pa Iye nyengo zonse, anthu inu, tsanulirani mitima yanu pamaso pake. Mulungu ndiye pothawirapo ife.


Ndipo Yehova adzakhala msanje kwa iye wokhalira mphanthi. Msanje m'nyengo za nsautso;


Kodi Iye wakulangiza mitundu ya anthu, ndiye wosadzudzula? Si ndiye amene aphunzitsa munthu nzeru?


iye adzakhala pamsanje; malo ake ochinjikiza adzakhala malinga amiyala; chakudya chake chidzapatsidwa kwa iye; madzi ake adzakhala chikhalire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa