Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 94:19 - Buku Lopatulika

19 Pondichulukira zolingalira zanga m'kati mwanga, zotonthoza zanu zikondweretsa moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Pondichulukira zolingalira zanga m'kati mwanga, zotonthoza zanu zikondweretsa moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Pamene nkhaŵa zikundichulukira, Inu mumasangalatsa mtima wanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Pamene nkhawa inakula mʼkati mwanga, chitonthozo chanu chinabweretsa chimwemwe mʼmoyo mwanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:19
12 Mawu Ofanana  

Ku malekezero a dziko lapansi ndidzafuulira kwa Inu, pomizika mtima wanga. Nditsogolereni kuthanthwe londiposa ine m'kutalika kwake.


Moyo wanga uzikumbukirabe nuwerama mwa ine.


Moyo wanga uti, Gawo langa ndiye Yehova; chifukwa chake ndidzakhulupirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa