Masalimo 94:18 - Buku Lopatulika18 Pamene ndinati, Literereka phazi langa, chifundo chanu, Yehova, chinandichirikiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pamene ndinati, Litereka phazi langa, chifundo chanu, Yehova, chinandichirikiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamene ndinkaganiza kuti, “Phazi langa likuterereka,” nkuti chikondi chanu chosasinthika chikundichirikiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndikanena kuti, “Phazi langa likuterereka,” chikondi chanu, Inu Yehova, chimandichirikiza. Onani mutuwo |