Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 94:17 - Buku Lopatulika

17 Akadapanda kukhala thandizo langa Yehova, moyo wanga ukadakhala kuli chete.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Akadapanda kukhala thandizo langa Yehova, moyo wanga ukadakhala kuli chete.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Chauta akadapanda kundithandiza, bwenzi posachedwa nditapita ku dziko lazii.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Yehova akanapanda kundithandiza, bwenzi nditakakhala msanga ku malo achete a imfa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:17
10 Mawu Ofanana  

Akufa salemekeza Yehova, kapena aliyense wakutsikira kuli chete:


Kundikankha anandikankha ndikadagwa; koma Yehova anandithandiza.


Iwo akukhulupirira Yehova akunga phiri la Ziyoni, losasunthika, likhazikika kosatha.


Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa;


Yehova, musandichititse manyazi; pakuti ndafuulira kwa Inu, oipa achite manyazi, atonthole m'manda.


Onani ikudza nthawi, ndipo yafika, imene mudzabalalitsidwa, yense ku zake za yekha, ndipo mudzandisiya Ine pa ndekha. Ndipo sindikhala pa ndekha, chifukwa Atate ali pamodzi ndi Ine,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa