Masalimo 91:7 - Buku Lopatulika7 Pambali pako padzagwa chikwi, ndi zikwi khumi padzanja lamanja lako; sichidzakuyandikiza iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pambali pako padzagwa chikwi, ndi zikwi khumi pa dzanja lamanja lako; sichidzakuyandikiza iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Anzako chikwi chimodzi angathe kuphedwa pambali pakopa, kapena zikwi khumi ku dzanja lako lamanja, koma iwe zoopsazo sizidzakukhudza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Anthu 1,000 atha kufa pambali pako, anthu 10,000 kudzanja lako lamanja, koma zoopsazo sizidzafika pafupi ndi iwe. Onani mutuwo |