Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 91:6 - Buku Lopatulika

6 kapena mliri woyenda mumdima, kapena chionongeko chakuthera usana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 kapena mliri woyenda mumdima, kapena chionongeko chakuthera usana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Sudzaopanso mliri wogwa usiku, kapena zoononga moyo masana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 kapena mliri umene umayenda mu mdima, kapena zowononga za pa nthawi ya masana.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 91:6
7 Mawu Ofanana  

Chomwecho Yehova anatumiza mliri pa Israele kuyambira m'mawa kufikira nthawi yoikika; ndipo anafapo anthu zikwi makumi asanu ndi awiri kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.


Ndipo kunali, usiku womwewo mthenga wa Yehova anatuluka, nakantha m'misasa ya Aasiriya zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza zisanu, ndipo pouka anthu mamawa, taonani, onsewo ndi mitembo.


Ndipo anaima pakati pa akufa ndi amoyo; ndi mliri unaleka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa