Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 90:16 - Buku Lopatulika

16 Chochita Inu chioneke kwa atumiki anu, ndi ulemerero wanu pa ana ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Chochita Inu chioneke kwa atumiki anu, ndi ulemerero wanu pa ana ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Mulole kuti ntchito zanu ziwoneke kwa atumiki anu, mphamvu zanu zaulemerero ziwoneke kwa ana ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ntchito zanu zionetsedwe kwa atumiki anu, kukongola kwanu kwa ana awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 90:16
10 Mawu Ofanana  

Mulungu, tidamva m'makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, za ntchitoyo mudaichita masiku ao, masiku akale.


Ndipo ndidzalingalira ntchito yanu yonse, ndi kulingalirabe zimene munazichita Inu.


Popeza Inu, Yehova, munandikondweretsa ndi kuchita kwanu, ndidzafuula mokondwera pa ntchito ya manja anu.


Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha; Yehova, tsitsimutsani ntchito yanu pakati pa zaka, pakati pa zaka mudziwitse; pa mkwiyo mukumbukire chifundo.


Ndipo ana anu amene mudanena, Adzakhala ogulidwa, ndi ana anu osadziwa chabwino kapena choipa ndi pano, iwo adzalowamo, ndidzawapatsa iwo ili, adzalilandira ndi iwo.


Thanthwe, ntchito yake ndi yangwiro; pakuti njira zake zonse ndi chiweruzo; Mulungu wokhulupirika ndi wopanda chisalungamo; Iye ndiye wolungama ndi wolunjika.


Ndipo taonani, lero lino ndilikumuka njira ya dziko lonse lapansi; ndipo mudziwa m'mitima yanu yonse, ndi m'moyo mwa inu nonse, kuti pa mau okoma onse Yehova Mulungu wanu anawanena za inu sanagwe padera mau amodzi; onse anachitikira inu, sanasowepo mau amodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa