Masalimo 89:9 - Buku Lopatulika9 Inu ndinu wakuchita ufumu pa kudzikuza kwa nyanja; pakuuka mafunde ake muwachititsa bata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Inu ndinu wakuchita ufumu pa kudzikuza kwa nyanja; pakuuka mafunde ake muwachititsa bata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mumalamulira nyanja yaukali. Mafunde ake akakwera, Inu mumaŵakhalitsa bata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mumalamula nyanja ya mafunde awukali; pamene mafunde ake awundana Inu mumawakhalitsa bata. Onani mutuwo |