Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 89:7 - Buku Lopatulika

7 Ndiye Mulungu, ayenera kumuopa kwambiri mu upo wa oyera mtima, ndiye wochititsa mantha koposa onse akumzinga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndiye Mulungu, ayenera kumuopa kwambiri m'upo wa oyera mtima, ndiye wochititsa mantha koposa onse akumzinga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Mulungu ndiye amene amamuwopa mu msonkhano wa anthu oyera mtima, ndiye wamkulu ndi wolemekezeka pakati pa onse omzungulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Mu msonkhano wa oyera mtima Mulungu amaopedwa kwambiri; Iye ndiye wochititsa mantha kupambana onse amene amuzungulira.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 89:7
17 Mawu Ofanana  

Akunga Yehova Mulungu wathu ndani? Amene akhala pamwamba patali,


Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu.


Pakuti Yehova Wam'mwambamwamba ndiye woopsa; ndiye mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.


Pakati pa milungu palibe wina wonga Inu, Ambuye; ndipo palibe ntchito zonga zanu.


Mudzafanizira Mulungu ndi yani tsopano, kapena kumyerekeza ndi chithunzithunzi chotani?


Mudzandifanizira Ine ndi yani tsono, kuti ndilingane naye, ati Woyerayo.


Pakuti zonsezi mkono wanga wazilenga, momwemo zonsezi zinaoneka, ati Yehova; koma ndidzayang'anira munthu uyu amene ali waumphawi, ndi wa mzimu wosweka, nanthunthumira ndi mau anga.


Koma Yehova ndiye Mulungu woona; ndiye Mulungu wamoyo, mfumu yamuyaya; pa mkwiyo wake dziko lapansi lidzanthunthumira, ndi amitundu sangapirire ukali wake.


Wosaopa Inu ndani, Mfumu ya amitundu? Pakuti kukuopani ndi kwanu; pakuti mwa anzeru onse a amitundu, ndi m'maufumu ao onse, mulibe akunga Inu.


Ndipo Mose anati kwa Aroni, Ichi ndi chimene Yehova ananena, ndi kuti, Mwa iwo akundiyandikiza ndipatulidwa Ine, ndi pamaso pa anthu onse ndilemekezedwa. Ndipo Aroni anakhala chete.


Ndipo musamaopa amene akupha thupi, koma moyo sangathe kuupha; koma makamaka muope Iye, wokhoza kuononga moyo ndi thupi lomwe muGehena.


Ndipo anadza mantha aakulu pa Mpingo wonse, ndi pa onse akumva izi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa