Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 89:6 - Buku Lopatulika

6 Pakuti kuli yani kuthambo timlinganize ndi Yehova? Afanana ndi Yehova ndani mwa ana a amphamvu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Pakuti kuli yani kuthambo timlinganize ndi Yehova? Afanana ndi Yehova ndani mwa ana a amphamvu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Kodi ndani mu mlengalenga angathe kulingana ndi Chauta? Ndani pakati pa akumwamba amafanafana naye?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pakuti ndani mu mlengalenga angalingane ndi Yehova? Ndani wofanana ndi Yehova pakati pa zolengedwa zakumwamba?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 89:6
10 Mawu Ofanana  

Akunga Yehova Mulungu wathu ndani? Amene akhala pamwamba patali,


Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu.


Inu, Yehova, Mulungu wanga, zodabwitsa zanu mudazichita nzambiri, ndipo zolingirira zanu za pa ife; palibe wina wozifotokozera Inu; ndikazisimba ndi kuzitchula, zindichulukira kuziwerenga.


Udzitamandiranji ndi choipa, chiphona iwe? Chifundo cha Mulungu chikhala tsiku lonse.


Chilungamo chanunso, Mulungu, chifikira kuthambo; Inu amene munachita zazikulu, akunga Inu ndani, Mulungu?


Ndili ndi yani Kumwamba, koma Inu? Ndipo padziko lapansi palibe wina wondikonda koma Inu.


Pakati pa milungu palibe wina wonga Inu, Ambuye; ndipo palibe ntchito zonga zanu.


Yehova, Mulungu wa makamu, wamphamvu ndani wonga Inu, Yehova? Ndipo chikhulupiriko chanu chikuzingani.


Afanana ndi Inu ndani mwa milungu, Yehova? Afanana ndi Inu ndani, wolemekezedwa, woyera, woopsa pomyamika, wakuchita zozizwa?


Chifukwa palibe akunga Inu, Yehova; muli wamkulu, ndipo dzina lanu lili lalikulu ndi lamphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa