Masalimo 88:9 - Buku Lopatulika9 Diso langa lapuwala chifukwa cha kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; nditambalitsira manja anga kwa Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Diso langa lapuwala chifukwa cha kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; nditambalitsira manja anga kwa Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 M'maso mwanga mwada ndi chisoni. Tsiku ndi tsiku ndimakuitanani, Inu Chauta, Ndimakweza manja anga kwa Inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 maso anga ada ndi chisoni. Ndimayitana Inu Yehova tsiku lililonse; ndimakweza manja anga kwa Inu. Onani mutuwo |