Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 88:7 - Buku Lopatulika

7 Mkwiyo wanu utsamira pa ine, ndipo munandizunza ine ndi mafunde anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Mkwiyo wanu utsamira pa ine, ndipo munandizunza ine ndi mafunde anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Mkwiyo wanu ukundipsinja, mukundimiza ndi mafunde anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ukali wanu ukundipsinja kwambiri, mwandiopseza kwambiri ndi mafunde anu onse. Sela

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 88:7
14 Mawu Ofanana  

Ndipo mutu wanga ukadzikweza, mundisaka ngati mkango; mubweranso ndi kudzionetsera modabwitsa kwa ine.


Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilowa, mzimu wanga uwumwa ulembe wake; zoopsa za Mulungu zindindandira nkhondo.


chifukwa cha ukali wanu ndi kuzaza kwanu; popeza munandinyamula ndipo munandigwetsa.


Chifukwa usana ndi usiku dzanja lanu linandilemera ine; uwisi wanga unasandulika kuuma kwa malimwe.


Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu, ndipo musandilange moopsa m'mtima mwanu.


Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, pa mkokomo wa matiti anu; mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.


Ndalema ndi kufuula kwanga; kum'mero kwauma gwaa! M'maso mwanga mwada poyembekeza Mulungu wanga.


Pakuti tionongeka mu mkwiyo wanu; ndipo m'kuzaza kwanu tiopsedwa.


Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza.


Ndipo ndinati, Ndatayika ndichoke pamaso panu; koma ndidzapenyanso Kachisi wanu wopatulika.


Iye amene akhulupirira Mwanayo ali nao moyo wosatha; koma iye amene sakhulupirira Mwanayo sadzaona moyo, koma mkwiyo wa Mulungu ukhala pa iye.


amene anasenza machimo athu mwini yekha m'thupi mwake pamtanda, kuti ife, titafa kumachimo, tikakhale ndi moyo kutsata chilungamo; ameneyo mikwingwirima yake munachiritsidwa nayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa