Masalimo 88:10 - Buku Lopatulika10 Kodi mudzachitira akufa zodabwitsa? Kodi adzaukanso otisiyawo, ndi kukulemekezani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Kodi mudzachitira akufa zodabwitsa? Kodi adzaukanso otisiyawo, ndi kukulemekezani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Kodi zodabwitsa mumachitira anthu akufa? Kodi iwowo nkuuka kuti akutamandeni? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kodi mumaonetsa zozizwitsa zanu kwa anthu akufa? Kodi iwo amene afa amaukanso ndi kutamanda Inu? Sela Onani mutuwo |