Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 87:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo adzanena za Ziyoni, uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo; ndipo Wam'mwambamwamba ndiye adzaukhazikitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo adzanena za Ziyoni, uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo; ndipo Wam'mwambamwamba ndiye adzaukhazikitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Koma ponena za Ziyoni adzati, “Onse adabadwira kumeneko,” chifukwa Wopambanazonse mwini wake ndiye amene adzaulimbitsa mzindawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndithudi, za Ziyoni adzanena kuti, “Uyu ndi uyo anabadwira mwa iye, ndipo Wammwambamwamba adzakhazikitsa iyeyo.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 87:5
14 Mawu Ofanana  

Monga tidamva, momwemo tidapenya m'mzinda wa Yehova wa makamu, m'mzinda wa Mulungu wathu, Mulungu adzaukhazikitsa kunthawi yamuyaya.


Tidalingalira zachifundo chanu, Mulungu, m'kati mwa Kachisi wanu.


Pozungulira pake ndipo mikono zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, ndi dzina la mzindawo kuyambira tsiku ilo lidzakhala, Yehova ali pomwepo.


Ndiponso Ine ndinena kwa iwe, kuti iwe ndiwe Petro, ndipo pa thanthwe ili ndidzakhazika Mpingo wanga; ndipo makomo a dziko la akufa sadzagonjetsa uwo.


Ndipo tidzatani ndi zinthu izi? Ngati Mulungu ali ndi ife, adzatikaniza ndani?


Ndipo ndinene chiyaninso? Pakuti idzandiperewera nthawi ndifotokozere za Gideoni, Baraki, Samisoni, Yefita; za Davide, ndi Samuele ndi aneneri;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa