Masalimo 86:17 - Buku Lopatulika17 Mundichitire chizindikiro choti chabwino; kuti ondida achione, nachite manyazi, popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Mundichitire chizindikiro choti chabwino; kuti ondida achione, nachite manyazi, popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mundiwonetse chizindikiro chakuti mumandikomera mtima, kuti odana nane achite manyazi. Adzaona kuti Inu Chauta mwandithandiza ndi kundilimbitsa mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mundionetse chizindikiro cha ubwino wanu kuti adani achione ndi kuchititsidwa manyazi, pakuti Yehova mwandithandiza ndi kunditonthoza. Onani mutuwo |