Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 86:13 - Buku Lopatulika

13 Pakuti chifundo chanu cha pa ine nchachikulu; ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Pakuti chifundo chanu cha pa ine nchachikulu; ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Paja chikondi chanu chosasinthika kwa ine nchachikulu, Mwandipulumutsa ku malo akuya a anthu akufa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu kwa ine; mwandipulumutsa ku malo ozama a manda.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 86:13
17 Mawu Ofanana  

kuti amletse angaonongeke, ndi moyo wake ungatayike ndi lupanga.


Inde wasendera kufupi kumanda, ndi moyo wake kwa akuononga.


pamenepo Mulungu amchitira chifundo, nati, Mlanditse, angatsikire kumanda, Ndampezera dipo.


Koma anandiombola ndingatsikire kumanda, ndi moyo wanga udzaona kuunika.


Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.


Pakuti munalanditsa moyo wanga kuimfa, maso anga kumisozi, mapazi anga, ndingagwe.


Pakuti simudzasiya moyo wanga kumanda; simudzalola wokondedwa wanu avunde.


Yehova munabweza moyo wanga kumanda, munandisunga ndi moyo, kuti ndingatsikire kudzenje.


Imbirani Yehova, inu okondedwa ake, ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake.


Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa, simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe? Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu m'kuunika kwa amoyo.


Pakuti chifundo chanu nchachikulu kufikira m'mwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.


Munandiika kunsi kwa dzenje, kuli mdima, kozama.


Taonani, ndinali ndi zowawa zazikulu, chifukwa cha mtendere wanga; Koma Inu mokonda moyo wanga, munaupulumutsa m'dzanja la chivundi, Pakuti mwaponya m'mbuyo mwanu machimo anga onse.


Ndipo anansi ake ndi abale ake anamva kuti Ambuye anakulitsa chifundo chake pa iye; nakondwera naye pamodzi.


ndi kulindirira Mwana wake achokere Kumwamba, amene anamuukitsa kwa akufa, Yesu, wotipulumutsa ife kumkwiyo ulinkudza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa