Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 84:8 - Buku Lopatulika

8 Yehova Mulungu wa makamu, imvani pemphero langa. Tcherani khutu, Mulungu wa Yakobo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Yehova Mulungu wa makamu, imvani pemphero langa. Tcherani khutu, Mulungu wa Yakobo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Inu Chauta, Mulungu Wamphamvuzonse, imvani pemphero langa. Tcherani khutu, Inu Mulungu wa Yakobe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Imvani pemphero langa, Inu Yehova Mulungu Wamphamvuzonse; mvereni Inu Mulungu wa Yakobo. Sela

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 84:8
4 Mawu Ofanana  

Koma wolungama asungitsa njira yake, ndi iye wa manja oyera adzakulabe mumphamvu.


Ndinu Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Israele. Ukani kukazonda amitundu onse, musachitire chifundo mmodzi yense wakuchita zopanda pake monyenga.


koma iwo amene alindira Yehova adzatenganso mphamvu; adzauluka pamwamba ndi mapiko monga ziombankhanga; adzathamanga koma osalema; adzayenda koma osalefuka.


Amuna onse azioneka pamaso pa Yehova Mulungu wanu m'malo amene Iye adzasankha, katatu m'chaka; pa chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa, pa chikondwerero cha masabata, ndi pa chikondwerero cha Misasa; ndipo asaoneke pamaso pa Yehova opanda kanthu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa