Masalimo 84:6 - Buku Lopatulika6 Popyola chigwa cha kulira misozi achiyesa cha akasupe; inde mvula ya chizimalupsa ichidzaza ndi madalitso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Popyola chigwa cha kulira misozi achiyesa cha akasupe; inde mvula ya chizimalupsa ichidzaza ndi madalitso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Akamadutsa chigwa cha Baka chopanda madzi, amachisandutsa malo a akasupe, mvula yachizimalupsa imachidzaza ndi zithaphwi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pamene akudutsa chigwa cha Baka, amachisandutsa malo a akasupe; mvula ya chizimalupsa imadzazanso mayiwe ake. Onani mutuwo |