Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:68 - Buku Lopatulika

68 koma anasankha fuko la Yuda, Phiri la Ziyoni limene analikonda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

68 koma anasankha fuko la Yuda, Phiri la Ziyoni limene analikonda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

68 Koma adasankhula fuko la Yuda, ndiponso phiri la Ziyoni limene amalikonda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

68 Koma anasankha fuko la Yuda, phiri la Ziyoni limene analikonda.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:68
7 Mawu Ofanana  

Komatu Yehova Mulungu wa Israele anasankha ine m'nyumba yonse ya atate wanga, ndikhale mfumu ya Israele kosatha; pakuti anasankhiratu Yuda akhale mtsogoleri, ndi m'nyumba ya Yuda nyumba ya atate wanga, ndi mwa ana a atate wanga ndinamkomera ndine, andilonge ufumu wa Israele yense;


Koma ndinasankha Yerusalemu, kuti dzina langa likhale komweko; ndinasankhanso Davide akhale mfumu ya anthu anga Israele.


Yehova akonda zipata za Ziyoni koposa zokhalamo zonse za Yakobo.


Ndipo Yehova ananena ndi Samuele, Iwe ukuti ulire chifukwa cha Saulo nthawi yotani, popeza Ine ndinamkana kuti asakhale mfumu ya Israele? Dzaza nyanga yako ndi mafuta, numuke, ndidzakutumiza kwa Yese wa ku Betelehemu; pakuti ndinadzionera mfumu pakati pa ana ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa