Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:66 - Buku Lopatulika

66 Ndipo anapanda otsutsana naye kumbuyo; nawapereka akhale otonzeka kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

66 Ndipo anapanda otsutsana naye kumbuyo; nawapereka akhale otonzeka kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

66 Tsono Mulungu adaŵapirikitsa adani ake, naŵachititsa manyazi anthaŵizonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

66 Iye anathamangitsa adani ake; anawachititsa manyazi ku nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:66
5 Mawu Ofanana  

Upenyerere aliyense wodzikuza, numtsitse, nupondereze oipa pomwe akhala.


ndipo ndidzakutengerani inu chitonzo chamuyaya, ndi manyazi amuyaya, amene sadzawailika.


Koma Yehova anavuta iwo a ku Asidodi ndi dzanja lake, nawaononga, nawazunza ndi mafundo, mu Asidodi ndi m'midzi yake.


Ndipo iwo aja anati, Tidzambwezera nsembe yopalamula yanji? Ndipo iwo anati, Mafundo asanu agolide, ndi mbewa zisanu zagolide, monga mwa chiwerengo cha mafumu a Afilisti; popeza kusauka kumodzi kunali pa inu nonse, ndi pa mafumu anu.


Ndipo pamene Samuele analikupereka nsembe yopserezayo, Afilisti anayandikira kuti aponyane ndi Aisraele; koma tsiku lomwe lija Yehova anagunda ndi kugunda kwakukulu pa Afilistiwo, nawapolonganitsa. Ndipo anakanthidwa pamaso pa Aisraele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa