Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:60 - Buku Lopatulika

60 ndipo anachokera chokhalamo cha ku Silo, chihemacho adachimanga mwa anthu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

60 ndipo anachokera chokhalamo cha ku Silo, chihemacho adachimanga mwa anthu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

60 Adasiya malo ake a Silo kumene ankakhala, adasiya hema limene ankakhalamo pakati pa anthu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

60 Anasiya nyumba ya ku Silo, tenti imene Iyeyo anayimanga pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:60
5 Mawu Ofanana  

Ndipo msonkhano wonse wa ana a Israele unasonkhana ku Silo, nuutsa komweko chihema chokomanako; ndipo dziko linawagonjera.


Ndipo munthuyo akakwera chaka ndi chaka kutuluka m'mzinda mwake kukalambira ndi kupereka nsembe kwa Yehova wa makamu mu Silo. Ndipo pomwepo panali ana aamuna awiri a Eli, ansembe a Yehova, ndiwo Hofeni ndi Finehasi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa